Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Moyo Wabwino Kwambiri

Moyo Wabwino Kwambiri

Achinyamata akhoza kuchita zambiri m’gulu la Yehova. Onerani vidiyo yakuti Moyo Wabwino Kwambiri, kuti muone zinthu zabwino zimene mtsikana wina dzina lake Cameron wachita. Kenako yankhani mafunso ali m’munsiwa. (Pitani pa jw.org/ny, pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA.)

  • Kodi Cameron amaona kuti chofunika kwambiri pamoyo wake n’chiyani?

  • Kodi anawonjezera liti utumiki wake nanga anachita bwanji zimenezi?

  • Kodi anakonzekera bwanji kukatumikira kudziko limene kukufunika olalikira ambiri?

  • Kodi ndi mavuto ati amene anakumana nawo kudziko limene anapita?

  • Kodi kulalikira kudera lachilendo kuli ndi ubwino wotani?

  • Kodi Cameron wadalitsidwa bwanji?

  • N’chifukwa chiyani tinganene kuti munthu amene akutumikira Yehova amakhala ndi moyo wabwino kwambiri?

  • Kodi ndi zinthu zina ziti zimene achinyamata angachite m’gulu la Yehova?