Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

February 1-7

NEHEMIYA 1-4

February 1-7
  • Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Konzekerani Zitsanzo za Ulaliki za Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani kavidiyo kosonyeza zitsanzo za ulaliki kenako kambiranani mfundo zimene mwaphunzirapo. Fotokozani zimene wofalitsa wachita kuti adzapange ulendo wobwereza. Limbikitsani omvera kuti alembe ulaliki umene angakonde kugwiritsa ntchito.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 103

  • Konzani Zoti Mudzachite Upainiya Wothandiza M’mwezi wa March Kapena April: (15 min.) Nkhani yokambirana. Gwiritsani ntchito mfundo zimene zili m’nkhani yakuti, “Zimene Mungachite Kuti Mudzasangalale M’nyengo ya Chikumbutso.” (km 2/14 2) Limbikitsani omvera kuti ayambe kukonzekera. (Miy. 21:5) Kenako funsani ofalitsa awiri amene anachitapo upainiya wothandiza kuti afotokoze mavuto amene anapirira komanso zosangalatsa zimene anapeza?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 25 ndime 9-16 (30 min.)

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 135 ndi Pemphero