Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Zimene Tinganene

Zimene Tinganene

●○○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi mukuganiza kuti tingapeze kuti malangizo omwe angatithandize kuti tizikhala osangalala?

Lemba: Sal. 1:1, 2

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi kukonda ndalama komanso chuma kungatibweretsere mavuto otani?

○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA

Funso: Kodi kukonda ndalama komanso chuma kungatibweretsere mavuto otani?

Lemba: 1 Tim. 6:9, 10

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi kukhala wosangalala kuli ndi ubwino wotani?

○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI

Funso: Kodi kukhala wosangalala kuli ndi ubwino wotani?

Lemba: Miy. 17:22

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tingatani kuti tizisangalalabe m’banja ngakhale tikukumana ndi mavuto?