Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 26

Kufanana Komanso Kusiyana Komwe Kulipo Pakati pa Mwambo wa Pasika ndi Chikumbutso

Kufanana Komanso Kusiyana Komwe Kulipo Pakati pa Mwambo wa Pasika ndi Chikumbutso

26:18

Tchulani zinthu zimene zili pa chithunzipa.

Pa zinthu zimenezi, kodi ndi zinthu ziti zomwe zimagwiritsidwanso ntchito pa mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye?