Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo?

Baibulo likuthandiza anthu mamiliyoni ambiri padziko lonse kupeza mayankho a mafunso ofunika kwambiri. Kodi inunso mukufuna kuthandizidwa?

Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji?

A Mboni za Yehova padziko lonse lapansi amadziwika bwino chifukwa cha ntchito yawo yophunzitsa anthu Baibulo kwaulere. Onani mmene amaphunzitsira.

Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?

Onani mkati mwa Nyumba ya Ufumu kuti mudziwe zimene zimachitika.

Pemphani Munthu Woti Aziphunzira Nanu

Phunzirani kwaulere mfundo za m’Baibulo pa nthawi ndi malo amene mukufuna.

Misonkhano ya Mpingo ya Mboni za Yehova

Dziwani malo amene timasonkhana komanso mmene timalambirira Mulungu.

Mfundo Zachidule​—Padziko Lonse

  • 240—Mayiko amene a Mboni za Yehova amalambira Mulungu

  • 8,340,982—Mboni za Yehova padziko lonse

  • 10,115,264—Maphunziro a Baibulo aulere

  • 20,085,142—Anthu amene anapezeka pa mwambo wokumbukira imfa ya Yesu Khristu

  • 119,485—Mipingo