Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Masewero a Nkhani za M’Baibulo

Koperani masewero a nkhani za m’Baibulo ndipo mungapeze phunziro lofunika kwambiri m’masewero amenewa. Mungaphunzirenso mfundo zina zofunika kwambiri zokhudza anthu otchulidwa m’Baibulo komanso zinthu zina zomwe zinachitika. Mungapzenso zinthu zina zongomvetsera pa webusaiti yathu.

Sankhani chinenero chimene mukufuna pa kabokosi ka zinenero, kenako dinani kabatani ka Fufuzani kuti muone masewero omwe alipo m’chinenerocho. Lembani mawu amodzi kapena awiri a dzina la sewero limene mukufuna.

Pepani, panopa pawebusaitiyi palibe zimene mukufunazi m'Chichewa.

Mungapeze za m'Chichewa pamasamba awa: