Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani!

Magazini athu ofotokoza za m’Baibulo akupezeka m’zinenero zoposa 150 kuphatikizapo m’chinenero chamanja ndipo mungathe kuwakopera. Magazini ya Nsanja ya Olonda imatisonyeza kugwirizana kwa zinthu zomwe zikuchitika m’dzikoli ndi maulosi a m’Baibulo. Magaziniyi imalimbikitsa anthu ndi uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu komanso imalimbikitsa kuti anthu azikhulupirira Yesu Khristu. Magazini ya Galamukani! imatiuza mfundo zomwe zingatithandize kupirira mavuto a masiku ano ndiponso imatilimbikitsa kuti tizidalira lonjezo la Mlengi wathu lakuti tiziyembekezera dziko latsopano limene mudzakhala mtendere.

Sankhani chinenero chimene mukufuna pa kabokosi ka zinenero, kenako dinani kabatani ka Fufuzani kuti muone magazini amene alipo m’chinenerocho.

ONANI
Ngati Kalenda
Mumndandanda

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

August 2017

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)