Pitani ku nkhani yake

Baibulo la pa Intaneti

Onerani Baibulo pa intaneti kapena pangani dawunilodi mavidiyo a Baibulo a chinenero chamanja. Mungapezenso Baibulo longomvetsera komanso lomwe mungathe kuwerenga pa intaneti. Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika ndi lolondola ndiponso losavuta kuwerenga. Baibulo lonseli, kapena mbali yake chabe, lasindikizidwa m’zinenero zoposa 120 kuphatikizapo m’zinenero zina zamanja, ndipo makope oposa 200 miliyoni afalitsidwa.

 

ONANI
Ngati Kalenda
Mumndandanda

BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA

Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika