Pitani ku nkhani yake

“Uthenga wabwino uwu wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu.”—Mateyu 24:14.

BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA

Kodi a Mboni za Yehova Mumawadziwa?

Ndife anthu ochokera m’mitundu, zikhalidwe ndiponso zinenero zosiyanasiyana, koma ndife ogwirizana kwambiri chifukwa cholinga chathu n’chimodzi. Cholinga chathu chachikulu n’kulemekeza Yehova, Mulungu wotchulidwa m’Baibulo ndiponso Mlengi wa zinthu zonse. Timayesetsa kutsanzira Yesu Khristu ndipo timanyadira kutchedwa Akhristu. Nthawi zonse aliyense wa ife amathera nthawi yake pothandiza ena kuphunzira Baibulo ndiponso za Ufumu wa Mulungu. Timatchedwa kuti Mboni za Yehova chifukwa choti timachitira umboni, kapena kuti kulalikira za Yehova Mulungu ndi Ufumu wake.

Fufuzani pa Webusaiti yathuyi. Werengani Baibulo pa Intaneti. Dziwani zambiri za ifeyo ndiponso zimene timakhulupirira.

Pemphani Munthu Woti Aziphunzira Nanu

Phunzirani kwaulere mfundo za m’Baibulo pa nthawi ndi malo amene mukufuna.

Mavidiyo Achikhristu

Mavidiyo a pawebusaitiyi amene angatithandize kuti tizikhulupirira kwambiri Mulungu.

Misonkhano ya Mpingo ya Mboni za Yehova

Dziwani malo amene timasonkhana komanso mmene timalambirira Mulungu.

Mabuku Ndiponso Zinthu Zina Zomwe Zilipo

Onani zinthu zomwe tangoziika kumene pa Intaneti komanso zina zomwe zilipo.